![](https://i0.wp.com/malawi24.com/wp-content/uploads/2024/07/UTM-scaled.webp?fit=2560%2C1920&ssl=1)
UTM yatuluka mgwirizano wa Tonse
Advertisement M’neneri wa chipani cha United Transformation Movement (UTM), a Felix Njawala, ati chipanichi chatuluka mu m’gwirizano omwe unalipo pakati pa chipanichi ndi zipani monga chipani cholamura cha Malawi Congress otchedwa Tonse Alliance. Izi …